1 Samueli 14:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano Sauli anafunsa Yonatani kuti: “Ndiuze, Wachita chiyani?”+ Poyankha, Yonatani anamuuza kuti: “Zoonadi, ndalawa uchi pang’ono kunsonga ya ndodo imene ili m’manja mwangayi.+ Ndiye ndiphenitu!” Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
43 Tsopano Sauli anafunsa Yonatani kuti: “Ndiuze, Wachita chiyani?”+ Poyankha, Yonatani anamuuza kuti: “Zoonadi, ndalawa uchi pang’ono kunsonga ya ndodo imene ili m’manja mwangayi.+ Ndiye ndiphenitu!”
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+