Miyambo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya oipa ili ngati mdima.+ Iwo sadziwa chimene chimawapunthwitsa.+