Yobu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iwo amafufuzafufuza mu mdima+ mopanda kuwala,Kuti awachititse kuyendayenda ngati munthu woledzera.+ Yesaya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akhale ngati malo opatulika.+ Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli, iye akhale ngati mwala wopunthwitsa ndiponso ngati mwala wokhumudwitsa.+ Akhalenso ngati msampha ndi khwekhwe kwa anthu okhala mu Yerusalemu.+ Mateyu 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alekeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Chotero ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera m’dzenje.”+
25 Iwo amafufuzafufuza mu mdima+ mopanda kuwala,Kuti awachititse kuyendayenda ngati munthu woledzera.+
14 Iye akhale ngati malo opatulika.+ Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli, iye akhale ngati mwala wopunthwitsa ndiponso ngati mwala wokhumudwitsa.+ Akhalenso ngati msampha ndi khwekhwe kwa anthu okhala mu Yerusalemu.+
14 Alekeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Chotero ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera m’dzenje.”+