Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Njira ya oipa ili ngati mdima.+ Iwo sadziwa chimene chimawapunthwitsa.+

  • Yesaya 28:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+

  • Mateyu 13:57
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena m’nyumba mwake, koma kwina.”+

  • Luka 20:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Aliyense wogwera pamwala umenewo adzaphwanyika.+ Ndipo aliyense amene mwalawo udzamugwere,+ udzam’pereratu.”+

  • Aroma 9:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Chifukwa chiyani? Chifukwa chakuti iwo sanalitsatire mwa chikhulupiriro, koma malinga ndi kuganiza kwawo, analitsatira mwa ntchito.+ Iwo anakhumudwa “pamwala wokhumudwitsa”+

  • Aroma 9:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Inetu ndikuika mwala+ wopunthwitsa ndiponso mwala wokhumudwitsa+ m’Ziyoni, koma munthu wokhulupirira mwalawo sadzakhumudwa.”+

  • 1 Petulo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 komanso “mwala wopunthwitsa ndi thanthwe lokhumudwitsa.”+ Anthu amenewa akupunthwa chifukwa samvera mawu, ndipo anaikidwiratu kale kuti adzatero.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena