Yesaya 59:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri, ndipo zolungama sizikutipeza. Tinali kuyembekezera kuunika koma m’malomwake tikungoona mdima. Tinali kuyembekezera kuwala koma tikungoyendabe mu mdima wosatha.+ Yohane 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo Yesu anati: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pang’ono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima+ usakugwereni, pakuti woyenda mu mdima sadziwa kumene akupita.+
9 N’chifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri, ndipo zolungama sizikutipeza. Tinali kuyembekezera kuunika koma m’malomwake tikungoona mdima. Tinali kuyembekezera kuwala koma tikungoyendabe mu mdima wosatha.+
35 Pamenepo Yesu anati: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pang’ono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima+ usakugwereni, pakuti woyenda mu mdima sadziwa kumene akupita.+