Yesaya 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iwo adzabangulira nyamayo m’tsiku limenelo ngati mkokomo wa nyanja.+ Munthu adzayang’ana dzikolo n’kuona kuti muli mdima womvetsa chisoni.+ Ngakhale kuwala kudzasanduka mdima chifukwa cha mvula imene idzagwe m’dzikolo. Yesaya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+
30 Iwo adzabangulira nyamayo m’tsiku limenelo ngati mkokomo wa nyanja.+ Munthu adzayang’ana dzikolo n’kuona kuti muli mdima womvetsa chisoni.+ Ngakhale kuwala kudzasanduka mdima chifukwa cha mvula imene idzagwe m’dzikolo.
22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+