2 Mbiri 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’masiku amenewo, anthu sankayenda mwamtendere+ chifukwa panali zisokonezo zambiri pakati pa anthu onse okhala m’madera a m’dzikoli.+ Yeremiya 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Choncho, njira zawo zidzawakhalira ngati malo oterera+ amdima ndipo adzawakankhira m’njirazo moti adzagwa.”+ “Pakuti ndidzawagwetsera tsoka, tsiku la chilango chawo lidzafika,”+ watero Yehova. Yoweli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+
5 M’masiku amenewo, anthu sankayenda mwamtendere+ chifukwa panali zisokonezo zambiri pakati pa anthu onse okhala m’madera a m’dzikoli.+
12 “Choncho, njira zawo zidzawakhalira ngati malo oterera+ amdima ndipo adzawakankhira m’njirazo moti adzagwa.”+ “Pakuti ndidzawagwetsera tsoka, tsiku la chilango chawo lidzafika,”+ watero Yehova.
31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+