Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti nyenyezi zakumwamba ndi magulu a nyenyezi a Kesili+ sizidzawala. Dzuwa lidzachita mdima potuluka, ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.

  • Yoweli 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Dzuwa ndi mwezi zidzachita mdima, ndipo nyenyezi zidzasiya kuwala.+

  • Mateyu 24:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi+ sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndipo mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka.+

  • Maliko 13:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Koma m’masiku amenewo, chisautso chimenecho chikadzatha, dzuwa lidzachita mdima, ndipo mwezi sudzapereka kuwala kwake.

  • Luka 21:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Komanso, padzakhala zizindikiro padzuwa,+ mwezi ndi nyenyezi. Padziko lapansi anthu a mitundu ina adzazunzika, ndipo adzathedwa nzeru chifukwa cha mkokomo wa nyanja+ ndi kuwinduka kwake.+

  • Chivumbulutso 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli*+ choluka ndi ubweya wa mbuzi yakuda, ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena