Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti nyenyezi zakumwamba ndi magulu a nyenyezi a Kesili+ sizidzawala. Dzuwa lidzachita mdima potuluka, ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.

  • Ezekieli 32:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Ndikadzakuzimitsa, ndidzaphimba kumwamba n’kuchititsa mdima nyenyezi zake. Dzuwa ndidzaliphimba ndi mitambo ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.+

  • Yoweli 2:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+

  • Machitidwe 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Dzuwa+ lidzasanduka mdima, ndipo mwezi udzasanduka magazi. Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi laulemerero la Yehova* lisanafike.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena