Zefaniya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+ Malaki 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tamverani anthu inu! Tsiku la Yehova lalikulu ndi lochititsa mantha lisanafike,+ ndidzakutumizirani mneneri Eliya.+
14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+
5 “Tamverani anthu inu! Tsiku la Yehova lalikulu ndi lochititsa mantha lisanafike,+ ndidzakutumizirani mneneri Eliya.+