Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 33:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipotu anthu awo otchuka adzalira mofuula m’misewu. Amithenga a mtendere+ adzalira momvetsa chisoni.

  • Yeremiya 48:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Matauni adzalandidwa. Malo ake odalirika adzalandidwa. Pa tsikulo, mitima ya amuna amphamvu a ku Mowabu idzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.’”+

  • Yoweli 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Kalanga ine! Tsiku lija likufika.+ Tsiku la Yehova lili pafupi.+ Tsikulo lidzafika ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuyonse.

  • Chivumbulutso 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena