Yoswa 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anapita kwa Yoswa kumsasa wa ku Giligala,+ ndipo anauza iye ndi amuna achiisiraeli kuti: “Ife tachokera kudziko lakutali kwambiri. Chonde, chitani nafe pangano.”+ Luka 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma akaona kuti sangakwanitse, mwamsanga amatumiza akazembe kwa mfumu inayo isanafike pafupi, kukapempha mtendere.+
6 Kenako anapita kwa Yoswa kumsasa wa ku Giligala,+ ndipo anauza iye ndi amuna achiisiraeli kuti: “Ife tachokera kudziko lakutali kwambiri. Chonde, chitani nafe pangano.”+
32 Koma akaona kuti sangakwanitse, mwamsanga amatumiza akazembe kwa mfumu inayo isanafike pafupi, kukapempha mtendere.+