Yoswa 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko. Yoswa 10:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atatero, Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye anabwerera kumsasa ku Giligala.+
10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko.