Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+ Mateyu 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kaya mukhulupirira kapena ayi, Yohane ndiye ‘Eliya woyembekezeka kubwera uja.’+ Maliko 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano anayamba kumufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya+ ayenera kubwera choyamba?”+
3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+
11 Tsopano anayamba kumufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya+ ayenera kubwera choyamba?”+