Malaki 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tamverani anthu inu! Tsiku la Yehova lalikulu ndi lochititsa mantha lisanafike,+ ndidzakutumizirani mneneri Eliya.+ Mateyu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ophunzirawo anamufunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya ayenera kubwera choyamba?”+ Mateyu 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe, ine ndikukuuzani kuti Eliya anabwera kale ndipo iwo sanamuzindikire koma anam’chitira zilizonse zimene iwo anafuna. Momwemonso iwo adzazunza Mwana wa munthu.”+
5 “Tamverani anthu inu! Tsiku la Yehova lalikulu ndi lochititsa mantha lisanafike,+ ndidzakutumizirani mneneri Eliya.+
10 Koma ophunzirawo anamufunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya ayenera kubwera choyamba?”+
12 Komabe, ine ndikukuuzani kuti Eliya anabwera kale ndipo iwo sanamuzindikire koma anam’chitira zilizonse zimene iwo anafuna. Momwemonso iwo adzazunza Mwana wa munthu.”+