-
Yobu 9:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Anapanga gulu la nyenyezi la Asi, gulu la nyenyezi la Kesili,
Gulu la nyenyezi la Kima+ ndi zipinda zamkati za Kum’mwera.
-
Amosi 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Yehova ndilo dzina+ la amene anapanga gulu la nyenyezi la Kima+ ndi gulu la nyenyezi la Kesili,+ amene amachititsa mdima wandiweyani+ kukhala kuwala kwa m’mamawa, amenenso amachititsa masana kukhala mdima ngati wausiku,+ amene amaitana madzi akunyanja kuti awakhuthulire panthaka ya dziko lapansi.+
-
-
-