Yobu 38:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kodi ungamange zingwe gulu la nyenyezi la Kima,Kapena kodi ungamasule zingwe za gulu la nyenyezi la Kesili?+ Yesaya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti nyenyezi zakumwamba ndi magulu a nyenyezi a Kesili+ sizidzawala. Dzuwa lidzachita mdima potuluka, ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.
31 Kodi ungamange zingwe gulu la nyenyezi la Kima,Kapena kodi ungamasule zingwe za gulu la nyenyezi la Kesili?+
10 Pakuti nyenyezi zakumwamba ndi magulu a nyenyezi a Kesili+ sizidzawala. Dzuwa lidzachita mdima potuluka, ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.