Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+ Amosi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taona! Yehova Mulungu wa makamu ndilo dzina+ la amene anapanga mapiri,+ analenga mphepo,+ amene amafotokozera munthu zimene akuganiza,+ amene amachititsa kuwala kwa m’bandakucha kukhala mdima+ ndiponso amene amaponda malo okwezeka a dziko lapansi.”+
18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+
13 Taona! Yehova Mulungu wa makamu ndilo dzina+ la amene anapanga mapiri,+ analenga mphepo,+ amene amafotokozera munthu zimene akuganiza,+ amene amachititsa kuwala kwa m’bandakucha kukhala mdima+ ndiponso amene amaponda malo okwezeka a dziko lapansi.”+