Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 65:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndi mphamvu zake, iye akukhazikitsa mapiri,+

      Iye wamanga mphamvu zochuluka m’chiuno mwake.+

  • Salimo 95:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Malo ozama kwambiri a dziko lapansi ali m’manja mwake,+

      Mapiri aatali nawonso ndi ake.+

  • Yesaya 40:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndani anayezapo madzi onse a m’nyanja pachikhatho cha dzanja lake?+ Ndani anayezapo kumwamba konse ndi dzanja lake?+ Ndani anayezapo fumbi lonse la padziko lapansi ndi mbale imodzi yokha yoyezera?+ Ndani anayezapo mapiri ndi muyezo, kapena ndani anayezapo zitunda pa sikelo?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena