Yoweli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+
31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+