Mateyu 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako ophunzira ake anafika ndi kumufunsa kuti: “Kodi mukudziwa kuti Afarisi akhumudwa ndi zimene mwanena zija?”+ 1 Petulo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 komanso “mwala wopunthwitsa ndi thanthwe lokhumudwitsa.”+ Anthu amenewa akupunthwa chifukwa samvera mawu, ndipo anaikidwiratu kale kuti adzatero.+
12 Kenako ophunzira ake anafika ndi kumufunsa kuti: “Kodi mukudziwa kuti Afarisi akhumudwa ndi zimene mwanena zija?”+
8 komanso “mwala wopunthwitsa ndi thanthwe lokhumudwitsa.”+ Anthu amenewa akupunthwa chifukwa samvera mawu, ndipo anaikidwiratu kale kuti adzatero.+