Maliko 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano atalowa m’nyumba ina kutali ndi khamu la anthulo, ophunzira ake anayamba kumufunsa za fanizo lija.+
17 Tsopano atalowa m’nyumba ina kutali ndi khamu la anthulo, ophunzira ake anayamba kumufunsa za fanizo lija.+