Yesaya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye adzakhala ngati malo opatulika,Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli,Adzakhala ngati mwala wopunthwitsa+Ndiponso ngati thanthwe lokhumudwitsa.Adzakhala ngati msampha komanso khwekhweKwa anthu okhala mu Yerusalemu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:14 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,10/1/2008, tsa. 5 Yesaya 1, tsa. 115
14 Iye adzakhala ngati malo opatulika,Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli,Adzakhala ngati mwala wopunthwitsa+Ndiponso ngati thanthwe lokhumudwitsa.Adzakhala ngati msampha komanso khwekhweKwa anthu okhala mu Yerusalemu.