Yesaya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akhale ngati malo opatulika.+ Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli, iye akhale ngati mwala wopunthwitsa ndiponso ngati mwala wokhumudwitsa.+ Akhalenso ngati msampha ndi khwekhwe kwa anthu okhala mu Yerusalemu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:14 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,10/1/2008, tsa. 5 Yesaya 1, tsa. 115
14 Iye akhale ngati malo opatulika.+ Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli, iye akhale ngati mwala wopunthwitsa ndiponso ngati mwala wokhumudwitsa.+ Akhalenso ngati msampha ndi khwekhwe kwa anthu okhala mu Yerusalemu.+