Yohane 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+ Afilipi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+ Akolose 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo chilichonse chimene mukuchita m’mawu kapena mu ntchito,+ muzichita zonse m’dzina la Ambuye Yesu,+ ndipo muziyamika+ Mulungu Atate kudzera mwa iye.
6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+
9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+
17 Ndipo chilichonse chimene mukuchita m’mawu kapena mu ntchito,+ muzichita zonse m’dzina la Ambuye Yesu,+ ndipo muziyamika+ Mulungu Atate kudzera mwa iye.