1 Akorinto 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye chifukwa chake, kaya mukudya kapena kumwa kapena mukuchita china chilichonse, chitani zonse kuti zibweretse ulemerero kwa Mulungu.+
31 Ndiye chifukwa chake, kaya mukudya kapena kumwa kapena mukuchita china chilichonse, chitani zonse kuti zibweretse ulemerero kwa Mulungu.+