Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba.

  • Akolose 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo chilichonse chimene mukuchita m’mawu kapena mu ntchito,+ muzichita zonse m’dzina la Ambuye Yesu,+ ndipo muziyamika+ Mulungu Atate kudzera mwa iye.

  • 1 Petulo 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ngati wina akulankhula, alankhule monga mwa mawu opatulika+ a Mulungu. Ngati wina akutumikira,+ atumikire modalira mphamvu imene Mulungu amapereka,+ kuti m’zinthu zonse Mulungu alemekezeke+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ulemerero+ ndi mphamvu, ndi zake mpaka muyaya. Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena