Mateyu 13:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena m’nyumba mwake, koma kwina.”+
57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena m’nyumba mwake, koma kwina.”+