Salimo 44:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti inu mwatiphwanya kumalo amene mimbulu imasonkhana,+Mwatiphimba ndi mdima wandiweyani.+