Salimo 74:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zizindikiro zathu sitinazione, ndipo palibenso mneneri amene watsala,+Pakati pathu palibe amene akudziwa kuti zikhala choncho mpaka liti. Ezekieli 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 akazi inu simupitiriza kuona masomphenya abodza+ ndipo simudzaloseranso zam’tsogolo.+ Ineyo ndidzapulumutsa anthu anga m’manja mwanu+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”+
9 Zizindikiro zathu sitinazione, ndipo palibenso mneneri amene watsala,+Pakati pathu palibe amene akudziwa kuti zikhala choncho mpaka liti.
23 akazi inu simupitiriza kuona masomphenya abodza+ ndipo simudzaloseranso zam’tsogolo.+ Ineyo ndidzapulumutsa anthu anga m’manja mwanu+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”+