Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Zingwe za imfa zinandikulunga,+

      Chikhamu cha anthu opanda pake chinali kundiopseza.+

  • Yesaya 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ndipo idzadutsa mu Yuda yense. Idzadutsa ngati madzi osefukira,+ ndipo idzafika mpaka m’khosi.+ Idzatambasula mapiko ake+ mpaka m’lifupi mwa dziko lako, iwe Emanueli.”+

  • Ezekieli 27:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “‘“Anthu okupalasa akupititsa pamadzi ozama.+ Mphepo ya kum’mawa yakuwononga pakatikati pa nyanja.+

  • Danieli 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Pambuyo pa milungu 62 imeneyi, Mesiya adzaphedwa+ ndipo sadzasiya kalikonse.+

      “Gulu lankhondo la mtsogoleri amene akubwera lidzawononga+ mzindawo ndi malo oyera.+ Malo oyera amenewo adzafafanizidwa ndi madzi osefukira, ndipo padzakhala nkhondo mpaka kumapeto. Mulungu wagamula kuti padzakhale chiwonongeko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena