Yesaya 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Yehovayo akupatsani chizindikiro anthu inu: Tamverani! Mtsikana+ adzatenga pakati+ ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli. Mateyu 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tamverani! Namwali+ adzatenga pakati ndipo adzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli,”+ lotanthauza “Mulungu Ali Nafe,”+ likamasuliridwa.
14 Choncho Yehovayo akupatsani chizindikiro anthu inu: Tamverani! Mtsikana+ adzatenga pakati+ ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli.
23 “Tamverani! Namwali+ adzatenga pakati ndipo adzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli,”+ lotanthauza “Mulungu Ali Nafe,”+ likamasuliridwa.