Mateyu 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tamverani! Namwali+ adzatenga pakati ndipo adzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli,”+ lotanthauza “Mulungu Ali Nafe,”+ likamasuliridwa. Luka 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera+ udzafika pa iwe, ndipo mphamvu ya Wam’mwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechinso, wodzabadwayo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+
23 “Tamverani! Namwali+ adzatenga pakati ndipo adzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli,”+ lotanthauza “Mulungu Ali Nafe,”+ likamasuliridwa.
35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera+ udzafika pa iwe, ndipo mphamvu ya Wam’mwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechinso, wodzabadwayo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+