Maliko 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anawayankha kuti: “Eliya adzabweradi choyamba ndi kubwezeretsa zinthu zonse.+ Koma n’chifukwa chiyani malemba amanena za Mwana wa munthu, kuti ayenera kukumana ndi mavuto ambiri,+ ndi kumuchita zinthu ngati munthu wopanda pake?+
12 Iye anawayankha kuti: “Eliya adzabweradi choyamba ndi kubwezeretsa zinthu zonse.+ Koma n’chifukwa chiyani malemba amanena za Mwana wa munthu, kuti ayenera kukumana ndi mavuto ambiri,+ ndi kumuchita zinthu ngati munthu wopanda pake?+