Luka 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Herode pamodzi ndi asilikali ake omulondera anamupeputsa.+ Anamuchitira zachipongwe+ mwa kumuveka chovala chonyezimira ndipo anamutumizanso kwa Pilato. Afilipi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+
11 Pamenepo Herode pamodzi ndi asilikali ake omulondera anamupeputsa.+ Anamuchitira zachipongwe+ mwa kumuveka chovala chonyezimira ndipo anamutumizanso kwa Pilato.
7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+