2 Mbiri 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’kupita kwa nthawi, Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri anabwera kudzamenyana naye. Iye anam’sautsa+ ndipo sanam’limbikitse. Yesaya 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye waukira Ayati.+ Wadutsa ku Migironi. Waika katundu wake ku Mikimasi.+
20 M’kupita kwa nthawi, Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri anabwera kudzamenyana naye. Iye anam’sautsa+ ndipo sanam’limbikitse.