Ezara 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nditangomva nkhani imeneyi, ndinang’amba zovala zanga+ n’kuyamba kuzula tsitsi la m’mutu mwanga+ ndi ndevu zanga, ndipo ndinakhala pansi ndili wokhumudwa ndi wachisoni kwambiri.+ Yesaya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+
3 Nditangomva nkhani imeneyi, ndinang’amba zovala zanga+ n’kuyamba kuzula tsitsi la m’mutu mwanga+ ndi ndevu zanga, ndipo ndinakhala pansi ndili wokhumudwa ndi wachisoni kwambiri.+
26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+