25 Ndiyeno ndinayamba kuwaimba mlandu ndi kuwatemberera.+ Ena mwa amuna amenewo ndinawamenya,+ kuwazula tsitsi ndi kuwalumbiritsa pamaso pa Mulungu kuti:+ “Musapereke ana anu aakazi kwa ana awo aamuna, ndipo musalole kuti ana awo aakazi akwatiwe ndi ana anu aamuna kapenanso inuyo.+