Deuteronomo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azim’kwapula+ pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikoti zogwirizana ndi choipa chimene wachita. Ezara 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Aliyense wosatsatira chilamulo cha Mulungu wako+ ndi chilamulo cha mfumu, azipatsidwa chiweruzo msangamsanga, kaya choti aphedwe,+ athamangitsidwe,+ alipitsidwe ndalama,+ kapena aikidwe m’ndende.”
2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azim’kwapula+ pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikoti zogwirizana ndi choipa chimene wachita.
26 Aliyense wosatsatira chilamulo cha Mulungu wako+ ndi chilamulo cha mfumu, azipatsidwa chiweruzo msangamsanga, kaya choti aphedwe,+ athamangitsidwe,+ alipitsidwe ndalama,+ kapena aikidwe m’ndende.”