Genesis 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano ndiwe wotembereredwa, ndipo ndikukupitikitsa m’dera limene nthaka+ yake yatsegula pakamwa ndi kulandira magazi a m’bale wako, amene iwe wakhetsa ndi manja ako.+
11 Tsopano ndiwe wotembereredwa, ndipo ndikukupitikitsa m’dera limene nthaka+ yake yatsegula pakamwa ndi kulandira magazi a m’bale wako, amene iwe wakhetsa ndi manja ako.+