Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 5:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iwo adzabangulira nyamayo m’tsiku limenelo ngati mkokomo wa nyanja.+ Munthu adzayang’ana dzikolo n’kuona kuti muli mdima womvetsa chisoni.+ Ngakhale kuwala kudzasanduka mdima chifukwa cha mvula imene idzagwe m’dzikolo.

  • Yesaya 50:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kumwamba ndimakuveka mdima+ ndipo chiguduli ndimachisandutsa chophimba chake.”+

  • Yoweli 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Limeneli ndi tsiku lamdima ndi lachisoni,+ tsiku lamitambo ndi lamdima wandiweyani. Tsikuli lili ngati mmene kuwala kwa m’bandakucha kumakhalira pamwamba pa mapiri.+

      “Pali mtundu wa anthu ambiri ndiponso amphamvu.+ Palibe mtundu wina umene ungafanane nawo kuyambira nthawi yakale+ ndipo sipadzakhalanso wina wofanana nawo ku mibadwomibadwo.

  • Yoweli 2:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “Ndidzachita zodabwitsa kuthambo+ ndi padziko lapansi. Ndidzachititsa kuti pakhale magazi, moto ndi utsi wokwera kumwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena