Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza kumwamba+ kuti m’dziko lonse la Iguputo mugwe mdima wandiweyani.”

  • Salimo 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+

      Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,

      Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+

  • Mateyu 27:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Kuyambira cha m’ma 12 koloko masana* kunagwa mdima+ m’dziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena