Ekisodo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni kuti, ‘Tambasula dzanja lako ndi kulozetsa ndodo+ yako kumitsinje, kungalande zochokera kumtsinje wa Nailo ndi kuzithaphwi, kuti achule atuluke mmenemo ndi kubwera pamtunda m’dziko lonse la Iguputo.’”
5 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni kuti, ‘Tambasula dzanja lako ndi kulozetsa ndodo+ yako kumitsinje, kungalande zochokera kumtsinje wa Nailo ndi kuzithaphwi, kuti achule atuluke mmenemo ndi kubwera pamtunda m’dziko lonse la Iguputo.’”