Ekisodo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Mose anatenga mkazi wake ndi ana ake ndi kuwakweza pabulu, ndi kuyamba ulendo wobwerera ku Iguputo. Komanso, Mose anatenga ndodo ya Mulungu woona m’dzanja lake.+ Ekisodo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero Mose anauza Yoswa* kuti:+ “Tisankhire amuna, ndipo upite nawo+ kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona m’dzanja langa.”+
20 Kenako Mose anatenga mkazi wake ndi ana ake ndi kuwakweza pabulu, ndi kuyamba ulendo wobwerera ku Iguputo. Komanso, Mose anatenga ndodo ya Mulungu woona m’dzanja lake.+
9 Zitatero Mose anauza Yoswa* kuti:+ “Tisankhire amuna, ndipo upite nawo+ kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona m’dzanja langa.”+