Yesaya 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+ Hoseya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+ Yoweli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+
4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+
3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+
10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+