Yesaya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+ Yesaya 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzikolo likulira, lafota.+ Lebanoni wachita manyazi, wanyala.+ Sharoni+ wakhala ngati chipululu ndipo Basana ndi Karimeli akuyoyola masamba awo.+ Yeremiya 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+ Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima. Hoseya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+
26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+
9 Dzikolo likulira, lafota.+ Lebanoni wachita manyazi, wanyala.+ Sharoni+ wakhala ngati chipululu ndipo Basana ndi Karimeli akuyoyola masamba awo.+
28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+
4 Njira zopita ku Ziyoni zikulira, chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+Zipata zake zonse zasiyidwa.+ Ansembe+ ake akuusa moyo.*Anamwali ake agwidwa ndi chisoni,+ ndipo iyeyo akumva kuwawa mumtima.
3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+