Yesaya 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse m’dziko n’kulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga dzikolo,+ n’kubalalitsa anthu okhalamo.+ Yesaya 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+
24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse m’dziko n’kulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga dzikolo,+ n’kubalalitsa anthu okhalamo.+
4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+