Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 24:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+

  • Yeremiya 4:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+

  • Yoweli 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+

  • Amosi 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pa chifukwa chimenechi dziko lidzagwedezeka,+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonselo lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo ndi kuwinduka, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena