Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 74:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Zizindikiro zathu sitinazione, ndipo palibenso mneneri amene watsala,+

      Pakati pathu palibe amene akudziwa kuti zikhala choncho mpaka liti.

  • Yeremiya 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova wa makamu wanena kuti: “Musamvere mawu a aneneri amene akulosera kwa anthu inu.+ Akukulimbikitsani kuchita zinthu zopanda pake.+ Iwo akulankhula masomphenya a mumtima mwawo+ osati ochokera m’kamwa mwa Yehova.+

  • Maliro 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Aneneri ako aona masomphenya achabechabe ndi opanda pake+ onena za iwe.

      Iwo sanaulule zolakwa zako kuti akuteteze n’cholinga choti usatengedwe kupita ku ukapolo,+

      Koma anali kuona masomphenya achabechabe ndi osocheretsa+ onena za iwe.

  • Ezekieli 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka kwa aneneri opusa,+ amene akungolosera zamumtima mwawo+ pamene sanaone chilichonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena