Miyambo 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wodalira mtima wake ndi wopusa,+ koma woyenda mwanzeru ndi amene adzapulumuke.+